LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 July tsa. 7
  • Kodi Munthu Wofunika Kwambili pa Umoyo Wanu N’ndani?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Munthu Wofunika Kwambili pa Umoyo Wanu N’ndani?
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Nkhani Zofanana
  • Gao 2
    Mvetselani kwa Mulungu
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 July tsa. 7

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MASALIMO 79-86

Kodi Munthu Wofunika Kwambili pa Umoyo Wanu N’ndani?

Wamasalimo aliza zeze

Amene analemba Salimo 83 ayenela kuti anali mbadwa ya Asafu Mlevi, ndipo ayenela kuti anakhalako panthawi imene Davide anali moyo. Salimo imeneyi inalembedwa pamene adani anali kuopseza anthu a Yehova.

83:1-5, 16

  • M’pemphelo lake, wamasalimoyu anakamba kwambili za dzina la Yehova ndi kulemekezeka kwa dzinalo m’malo mopempha kuti Yehova amuteteze

  • Masiku ano atumiki a Mulungu amakumana ndi mavuto ambili. Tikapilila ndi kukhala wokhulupilika, Yehova amalemekezeka

83:18

  • Yehova amafuna kuti tidziŵe dzina lake

  • Zocita zathu zizionetsa kuti Yehova ndiye munthu wofunika kwambili pa umoyo wathu

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani