LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 July tsa. 7
  • July 25-31

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • July 25-31
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 July tsa. 7

July 25-31

MASALIMO 79-86

  • Nyimbo 138 ndi Pemphelo

  • Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Kodi Munthu Wofunika Kwambili pa Umoyo Wanu N’ndani?”: (Mph. 10)

    • Sal. 83:1-5—Nkhani yofunika kwambili kwa ife ni yokhudza dzina la Yehova ndi ulamulilo wake (w08 10/15-CN, tsa. 13 ndime 7-8)

    • Sal. 83:16—Kukhulupilika ndi kupilila kwathu kumalemekezetsa dzina la Yehova (w08 10/15-CN, tsa. 15 ndime 16)

    • Sal. 83:17, 18—Yehova ndiye Munthu wofunika kwambili m’cilengedwe conse (w11 5/15-CN, tsa. 16 ndime 1-2; w08 10/15-CN, tsa. 15-16 ndime 17-18)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 8)

    • Sal. 79:9—Kodi vesi imeneyi itiphunzitsa ciani ponena za pemphelo? (w06 7/15-CN, tsa. 12 ndime 5)

    • Sal. 86:5—Kodi Yehova ni ‘wokonzeka bwanji kukhululuka’? (w06 7/15-CN, tsa. 12 ndime 9)

    • Kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ningaseŵenzetse mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibulo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Sal. 85:8–86:17

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 2 kapena zocepelapo) Uthenga Wabwino phunzilo 7 ndime 1

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Uthenga Wabwino phunzilo 7 ndime 3

  • Phunzilo la Baibulo: (Mph. 6 kapena zocepelapo) Uthenga Wabwino phunzilo 5 ndime 7-8

UMOYO WATHU WACIKHIRISTU

  • Nyimbo 111

  • Kodi Mulungu ali ndi Dzina?: (Mph. 15.) Yambani mwa kutambitsa vidiyo imene ili pa jw.org yakuti Kodi Mulungu Ali ndi Dzina?. (Pitani pa MABUKU > MABUKU NDI TUMABUKU. Ndiyeno pezani kabuku ka Uthenga Wabwino. Vidiyoyi ipezeka pansi pa kamutu kakuti “Kodi Mulungu Ndani?”) Pambuyo pake, kambilanani mafunso otsatila: Kodi tingaseŵenzetse bwanji vidiyo imeneyi mu ulaliki wamwayi, wapoyela, ndi wa nyumba ndi nyumba? Pamene munali kutambitsa anthu vidiyo imeneyi, Kodi panacitikako zabwino ziti zimene mungasimbeko? Ngati palibe vidiyo, sewenzetsani Zakumapeto pa masamba 195-197, m’buku la Zimene Baibo Imaphunzitsa.

  • Phunzilo la Baibulo la Mpingo: (Mph. 30) ia mutu. 20 ndime 14-26, ndi kubwelelamo pa tsa. 179

  • Kubwelelamo ndi Kuchulako za Mlungu Wotsatila (Mph. 3.)

  • Nyimbo 143 ndi Pemphelo.

    Cikumbutso: Lizani nyimboyi kamodzi. Pambuyo pake, mpingo uimbile pamodzi nyimbo yatsopanoyi.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani