September 5-11
SALIMO 119
Nyimbo 48 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Muzitsatila Cilamulo ca Yehova”: (Mph. 10)
Sal. 119:1-8—Kutsatila cilamulo ca Mulungu n’kumene kumatipatsa cimwemwe ceni-ceni (w05 4/15-CN, tsa. 10 ndime 3-4)
Sal. 119:33-40—Mawu a Mulungu amatithandiza kuti tikhale olimba mtima polimbana ndi ziyeso (w05 4/15-CN, tsa. 12 ndime 12)
Sal. 119:41-48—Kudziŵa molondola Mawu a Mulungu kumatithandiza kulalikila molimba mtima (w05 4/15-CN, tsa. 13 ndime 13-14)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 8)
Sal. 119:71—Kodi kuzunzidwa kungakhale kokoma m’njila yanji? (w06 9/1-CN, tsa. 14 ndime 4)
Sal. 119:96—Kodi mawu akuti, “Ndaona kuti zinthu zonse zabwino kwambili zili ndi malile” atanthauza ciani? (w06 9/1-CN, tsa. 14 ndime 5)
Kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani za Yehova?
Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ningaseŵenzetse mu ulaliki?
Kuŵelenga Baibulo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Sal. 119:73-93
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Konzekelani Maulaliki a Mwezi Uno: (Mph. 15) Kukambilana. Tambitsani mavidiyo a maulaliki acitsanzo, ndipo kambilanani mfundo zake. Limbikitsani ofalitsa kukonza ulaliki wawo.
UMOYO WATHU WACIKHIRISTU
“Mukapeza Mwana Panyumba”: (Mph. 5) Nkhani.
Zosoŵa za Pampingo: (Mph. 10) Ngati mufuna, mungakambilane zimene munaphunzila mu Buku Lapacaka. (yb16 masa. 59-62)
Phunzilo la Baibulo la Mpingo: (Mph. 30) ia nkhani 23 ndime 15-29, ndi kubwelelamo tsa. 204
Kubwelelamo ndi Kuchulako za Mlungu Wotsatila (Mph. 3)
Nyimbo 13 na Pemphelo