LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 October tsa. 4
  • October 17-23

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • October 17-23
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 October tsa. 4

October 17-23

MIYAMBO 12–16

  • Nyimbo 69 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Nzelu ni Yabwino Kwambili Kuposa Golide”: (Mph. 10)

    • Miy. 16:16, 17—Munthu wanzelu amaphunzila Mau a Mulungu ndi kuwaseŵenzetsa (w07 7/15 CN, tsa 8)

    • Miy. 16:18, 19—Munthu wanzelu amapewa kunyada ndi kudzikuza (w07 7/15 CN, tsa. 8-9)

    • Miy. 16:20-24—Munthu wanzelu amakamba mau olimbikitsa kwa ena (w07 7/15 CN, tsa. 9-10)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 8)

    • Miy. 15:15—Tingacite ciani kuti tizikhala osangalala kwambili pa umoyo wathu? (g11/13 tsa. 16)

    • Miy. 16:4—Kodi mfundo yakuti Yehova anapanga oipa “n’colinga” itanthauza ciani? (w07 5/15-CN, tsa. 18-19)

    • Kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ningaseŵenzetse mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibulo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Miy. 15:18 mpaka 16:6

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 2 kapena zocepelapo) Yoh. 11:11-14—Phunzitsani Coonadi. Itanilani munthuyo ku misonkhano ya kumapeto kwa mlungu.

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Gen. 3: 1-6; Aroma 5: 12—Phunzitsani Coonadi. Itanilani munthuyo ku misonkhano ya kumapeto kwa mlungu.

  • Phunzilo la Baibulo: (Mph. 6 kapena zocepelapo) bh tsa, 191 ndime 18-19—Itanilani wophunzilayo ku misonkhano.

UMOYO WATHU WACIKHIRISTU

  • Nyimbo 117

  • “Mmene Mungapelekele Mayankho Ogwila Mtima”: (Mph. 15) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Khala Bwenzi la Yehova—Konzekela Yankho Lako. Ndiyeno itanani ana ocepa kuti abwele ku pulatifomu ndipo afunseni kuti: N’zinthu zinai ziti zimene tiyenela kucita pokonzekela mayankho athu? N’cifukwa ciani sitiyenela kukhumudwa ngati sitinapatsidwe mwayi woyankha pa misonkhano?

  • Phunzilo la Baibulo la Mpingo: (Mph. 30) kr mutu 2 ndime 23-34

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Mlungu Wotsatila (Mph. 3)

  • Nyimbo 102 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani