LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 October tsa. 6
  • October 24-30

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • October 24-30
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 October tsa. 6

October 24-30

MIYAMBO 17-21

  • Nyimbo 76 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Muziyesetsa Kukhala Mwamtendele na Ena”: (Mph. 10)

    • Miy. 19:11—Muzikhala wodekha wina akakukhumudwitsani (w14 12/1-CN, masa. 12-13)

    • Miy. 18:13, 17; 21:13—Onetsetsani kuti mwamvetsetsa nkhani yonse (w11 8/15-CN, tsa. 30 ndime 11-14)

    • Miy. 17:9—Muzikhululukila amene akulakwilani (w11 8/15-CN, tsa. 31 ndime 17)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 8)

    • Miy. 17:5—Chulani cifukwa cimodzi cimene tifunika kusankhila zosangulutsa mwanzelu. (w10 11/15-CN, tsa. 6 ndime 17; w10 11/15-CN, tsa. 31 ndime 15)

    • Miy. 20:25—Kodi mfundo imeneyi igwila nchito bwanji ngati munthu ali pa cisumbali kapena m’cikwati? (w09 5/15-CN, masa. 15-16 ndime 12-13)

    • Kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibulo kwa mlungu uno zimene ningaseŵenzetse mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibulo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Miy. 18:14–19:10

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 2 kapena zocepelapo) Gaŵilani kapepa koitanila anthu ku misonkhano. (inv)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4 kapena zocepelapo) inv—Tsilizani na mau oonetsa kuti mufuna kumutambitsa vidiyo yakuti N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu?

  • Phunzilo la Baibulo: (Mph. 6 kapena zocepelapo) lv tsa. 57 ndime 14-15—Thandizani wophunzila kuona kuti afunika kuvala na kudzikonza moyenela popita kumisonkhano.

UMOYO WATHU WACIKHIRISTU

  • Nyimbo 77

  • Kukhazikitsa Mtendele Kumabweletsa Madalitso: (Mph. 15) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Kukhazikitsa Mtendele Kumabweletsa Madalitso. Ngati vidiyo kulibe, kambilanani nkhani ya mu Nsanja ya Mlonda ya May 2016, masamba 4-6, ndime 8-13, na zithunzi pa tsamba 13. Ndiyeno funsani mafunso awa: N’zinthu ziti zimene tifunika kupewa ngati takangana na munthu wina? Nanga ni madalitso ati amene tingapeze ngati tiseŵenzetsa malangizo a pa Miyambo 17:9 ndi Mateyu 5:23, 24?

  • Phunzilo la Baibulo la Mpingo: (Mph. 30) kr nkhani 2 ndime 35-40, bokosi na machati pa masa. 25-29

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Mlungu Wotsatila (Mph. 3)

  • Nyimbo 144 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani