CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | MIYAMBO 17-21
Muziyesetsa Kukhala Mwamtendele na Ena
Anthu a Yehova amacita khama kuti akhale pa mtendele na anzawo. Nthawi zina, iwo amakangana ndi kukhumudwitsana kwambili. Koma malangizo ocokela m’Mau a Mulungu amawathandiza.
Akasiyana maganizo, Akhiristu okhulupilika amasunga mtendele mwa . . .
19:11
kukhala odekha
18:13, 17
kuonetsetsa kuti amvetsetsa nkhani yonse
17:9
kukhululukila amene awalakwila