LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb16 December tsa. 6
  • December 19-25

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • December 19-25
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
mwb16 December tsa. 6

December 19-25

YESAYA 11-16

  • Nyimbo 143 na Pemphelo

  • Omau Oyamba (Mph. 3 kapena zocepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Dziko Lapansi Lidzadzala na Ŵanthu Odziwa Yehova”: (Mph. 10)

    • Yes. 11:3-5—Kudzakhala cilungamo mpaka muyaya (ip-1 160-161 ndime 9-11)

    • Yes. 11:6-8—Anthu na vinyama adzakhala pamtendele (w12 9/15 9-10 ndime 8-9)

    • Yes. 11:9—Mitundu yonse ya anthu idzaphunzila njila za Yehova (w16.06 tsa. 8 ndime 9; w13 6/1 7)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 8)

    • Yes. 11:1, 10—Kodi Yesu Khiristu angakhale bwanji “muzu wa Jese” na nthambi imene inamphuka “pacitsa ca Jese”? (w06 12/1 tsa. 9 ndime 6)

    • Yes. 13:17—Kodi Amedi anasuliza bwanji siliva ndipo sanakondwele na golide m’njila yanji? (w06 12/1 tsa.10 ndime 10)

    • Kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno kwaniphunzitsa ciani ine za Yehova?

    • Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno zimene ine ningaseŵenzetse mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Yes. 13:17–14:8

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 2 kapena zocepelapo) Yobu 34:10—Phunzitsani Coonadi.

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4 kapena zocepelapo) Mlal. 8:9; 1 Yoh. 5:19—Phunzitsani Coonadi.

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 6 kapena zocepelapo) lv tsa. 54 ndime 9—Onetsani mmene tingam’fikile pamtima wophunzila.

UMOYO WATHU WACIKHIRISTU

  • Nyimbo 24

  • “Maphunzilo Aumulungu Amagonjetsa Tsankho”: (Mph. 15) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Johny na Gideon: Anali Adani, Tsopano ni Abale (Yendani ku mavidiyo pa KUFUNSA MAFUNSO NA ZOCITIKA)..

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30.) kr nkhani 5 ndime 18-25, bokosi pa tsa. 57

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Mlungu Wotsatila (Mph. 3)

  • Nyimbo 151 na Pemphelo

    Cikumbutso: Lizani nyimbo yonse kamodzi, ndiyeno mpingo uyimbile pamodzi.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani