LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb17 February tsa. 6
  • February 27–March 5

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • February 27–March 5
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
mwb17 February tsa. 6

February 27–March 5

YESAYA 63-66

  • Nyimbo 19 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 mineti kapena kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Kumwamba Kwatsopano ndi Dziko Lapansi Latsopano Zidzabweletsa Cisangalalo Cacikulu”: (10 min.)

    • Yes. 65:17—“Zinthu zakale sizidzakumbukilidwanso” (ip-2 peji. 383 pala. 23)

    • Yes. 65:18, 19—Padzakhala cisangalalo cacikulu (ip-2 peji 384 pala. 25)

    • Yes. 65:21-23—Umoyo udzakhala wokhutilitsa, ndipo anthu adzakhala otetezeka (w12 9/15 peji 9 mapala. 4-5)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Yes. 63:5—Kodi mkwiyo wa Mulungu umam’cilikiza bwanji? (w07 1/15 peji 11 pala. 6)

    • Yes. 64:8—Kodi Yehova amaseŵenzetsa bwanji mphamvu zake monga Wotiumba? (w13 6/15 25 mapala. 3-5)

    • Kodi ine pacanga, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwaniphunzitsa ciani za Yehova?

    • Ni mfundo ziti pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino zimene ine pacanga ningaseŵenzetse mu ulaliki?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 mineti kapena kucepelapo) Yes. 63:1-10

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 mineti kapena kucepelapo) Aef. 5:33—Phunzitsani Coonadi.

  • Ulendo Wobwelelako: (4 mineti kapena kucepelapo) 1 Tim. 5:8; Tito 2:4, 5—Phunzitsani Coonadi.

  • Nkhani: (6 mineti kapena kucepelapo) Yes. 66:23; w06 11/1 peji 30-31 pala. 14-17—Mutu: Kusonkhana—Mbali Yosatha ya Kulambila Kwathu

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 129

  • ‘Kondwelani mu Ciyembekezo Canu’ (Yes. 65:17, 18; Aroma 12:12) (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Kondwelani ndi Ciyembekezo (yendani ku mavidiyo pa BAIBULO)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) kr nkhani 9 pala. 1-9, ndi chati papeji 89”

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 95 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani