May 1-7
YEREMIYA 32-34
Nyimbo 138 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 mineti kapena kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Cizindikilo Cakuti Isiraeli Adzabwezeletsedwa”: (10 min.)
Yer. 32:6-9, 15—Yehova anauza Yeremiya kugula munda monga cizindikilo cakuti Yehova adzabwezeletsa Isiraeli (it-1 peji 105 pala. 2)
Yer. 32:10-12—Yeremiya anatsatila ndondomeko yonse yogulila cinthu (w07 3/15 peji 11 pala. 3)
Yer. 33:7, 8—Yehova analonjeza kuti ‘adzayeletsa’ otengeledwa ku ukapolo (jr peji 152 mapa. 22-23)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Yer. 33:15—Kodi “mphukila” ya Davide n’ndani? (jr peji 173 pala. 10)
Yer. 33:23, 24—Ni “mabanja aŵili” ati amene akunenedwa palembali? (w07 3/15 peji 11 pala. 4)
Kodi imwe pacanu kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 mineti kapena kucepelapo) Yer. 32:1-12
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Konzekelani Maulaliki a Mwezi Uno: (15 min.) Kukambilana “Maulaliki a Citsanzo.” Tambitsani vidiyo imodzi imodzi ndipo kambilanani zimene mwaphunzilapo. Limbikitsani onse kuseŵenzetsa vidiyo yakuti “Kodi Cofunika N’ciani Kuti Banja Likhale Lamtendele?” pogaŵila kabuku kakuti N’zotheka Banja Lanu Kukhala Lacimwemwe (Yendani ku mavidiyo MISONKHANO NA UTUMIKI WATHU).
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Zofunikila za Mpingo: (15 min.) Apo ayi, kambilanani mfundo zimene mwaphunzila m’Buku Lapacaka. (yb16 mapeji 67-71)
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) kr nkhani 12 mapa. 1-8, na bokosi papeji 121”
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 23 na Pemphelo