Akuyeletsa pa Nyumba ya Ufumu ku Switzerland
Maulaliki a Citsanzo
NSANJA YA MLONDA
Mau oyamba: Nkhani ya amuna 4 okwela pa mahosi ni imodzi mwa nkhani zodziŵika kwambili m’buku la Chivumbulutso. Anthu ena amacita nayo mantha. Ena amacita nayo cidwi.
Lemba: Chiv: 1:3
Cogaŵila: Magaziniyi ya Nsanja ya Mlonda ifotokoza mmene nkhani ya amuna 4 okwela pa mahosi ingatipindulitsile.
PHUNZITSANI COONADI
Funso: Kodi n’zotheka kudziŵa zam’tsogolo?
Lemba: Yes. 46:10
Coonadi: Mulungu amatidziŵitsa zam’tsogolo kupitila m’Mau ake, Baibo.
N’ZOTHEKA BANJA LANU KUKHALA LACIMWEMWE
Mau Oyamba: Titambitsa kavidiyo aka kokhudza mabanja. [Tambitsani vidiyo yakuti Kodi Cofunika N’ciani Kuti Banja Likhale Lamtendele?.]
Cogaŵila: Ngati mungakonde kuŵelenga kabuku kamene aonetsa mu vidiyoyi ningakupatseni, kapena ningakuonetseni mmene mungakacitile dawunilodi pa webusaiti yathu.
KONZANI ULALIKI WANU
Funso:
Lemba:
Cogaŵila: