Agaŵila kabuku kakuti N’zotheka Banja Lanu Kukhala Lacimwemwe ku Georgia
Maulaliki a Citsanzo
NSANJA YA MLONDA
Funso: Kodi wopatsa mphatso wamkulu m’cilengedwe conse n’ndani?
Lemba: Yak. 1:17
Cogaŵila: Nsanja ya Mlonda iyi itionetsa mphatso yopambana zonse yocokela kwa Mulungu.
PHUNZITSANI COONADI
Funso: Kodi dzina la Mulungu n’ndani?
Lemba: Sal. 83:18
Coonadi: Dzina la Mulungu ni Yehova.
N’ZOTHEKA BANJA LANU KUKHALA LACIMWEMWE
Mau Oyamba: Titambitsako kavidiyo kokamba za banja. [Tambitsani kavidiyo kakuti N’zotheka Banja Lanu Kukhala Lacimwemwe—Mau Oyamba.]
Cogaŵila: Ngati mungakonde kuŵelengako kabuku kachulidwa mu vidiyo, ningakupatseni, olo ningakuonetseni mmene timacitila daunilodi pa webusaiti.
KONZANI ULALIKI WANU
Funso:
Lemba:
Cogaŵila: