CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
Yehova Saiŵala Cikondi Canu
TAMBITSANI VIDIYO YAKUTI YEHOVA SAIŴALA CIKONDI CANU, NDI KUKAMBILANA MAFUNSO AYA:
Ni mavuto anji amene amabwela na ukalamba?
Nanga ni khalidwe labwino liti limene limabwela na ukalamba?
Ngati ndinu wokalamba, kodi malemba a Levitiko 19:32 na Miyambo 16:31 amakulimbikitsani bwanji?
Kodi Yehova amawaona bwanji atumiki ake okalamba amene sacita zambili mu utumiki?
N’ciani cimene Yehova amafuna kuti tizicitabe olo kuti takalamba?
Kodi okalamba angalimbikitse bwanji acicepele?
Kodi m’bale kapena mlongo wokalamba anakulimbikitsani bwanji posacedwa?