May 22-28
YEREMIYA 44-48
Nyimbo 70 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 mineti kapena kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Leka ‘Kufuna-funa Zinthu Zazikulu’” (10 min.)
Yer. 45:2, 3—Maganizo olakwika a Baruki anam’pangitsa kuvutika mtima kwambili (jr peji 104-105 mapa. 4-6)
Yer. 45:4, 5a—Yehova anawongolela Baruki mokoma mtima (jr peji 103 pala. 2)
Yer. 45:5b—Baruki anapulumutsa moyo wake poika maganizo ake pa zinthu zofunika kwambili (w16.07 8 pala. 6)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Yer. 48:13—N’cifukwa ciani Amoabu ‘anacita manyazi ndi Kemosi’? (it-1 430)
Yer. 48:42—N’cifukwa ciani ciweluzo ca Yehova kwa Amoabu n’colimbitsa cikhulupililo? (it-2 peji 422 pala. 2)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 mineti kapena kucepelapo) Yer. 47:1-7
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (2 mineti kapena kucepelapo) hf—Yalani maziko a ulendo wobwelelako.
Ulendo Wobwelelako: (4 mineti kapena kucepelapo) hf—Yalani maziko a ulendo wotsatila.
Phunzilo la Baibo: (6 mineti kapena kucepelapo) lv peji 199 mapa. 9-10—Mwacidule, onetsani wophunzilayo mofufuzila zimene zingam’thandize pa ciyeso cimene akukumana naco.
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
Acicepele—Musamafune-fune Zinthu Zazikulu: (15 min.) Tambitsani vidiyo yakuti Acicepele Akufunsa—Moyo Wanga Nidzauseŵenzetsa Bwanji?—Kuganizila Zakumbuyo (yendani ku mavidiyo ACICEPELE).
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) kr mapeji 132-133, nkhani 13 mapa. 1-10
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 17 na Pemphelo