July 24-30
EZEKIELI 21-23
Nyimbo 99 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 mineti kapena kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Ufumuwo ni wa Uyo Ali Woyenelela Mwalamulo”: (10 min.)
Ezek. 21:25—“Mtsogoleli wa Isiraeli woipa” anali Mfumu Zedekiya (w07 7/1 peji 13 pala. 11)
Ezek. 21:26—Mzela wa mafumu ocokela mwa Davide olamulila mu Yerusalemu unali kudzatha (w11 8/15 peji 9 pala. 6)
Ezek. 21:27—Yesu Khristu ndiye “woyenelela mwalamulo” (w14 10/15 peji 10 pala. 14)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Ezek. 21:3—Kodi “lupanga” limene Yehova akusolola m’cimake n’ciani? (w07 7/1 peji 14 pala. 1)
Ezek. 23:49—Kodi mu caputa 23 akufotokozamo colakwa canji? Nanga titengapo phunzilo lanji? (w07 7/1 peji 14 pala. 6)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 mineti kapena kucepelapo) Ezek. 21:1-13
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (2 mineti kapena kucepelapo) fg—Chulani za vidiyo yakuti Kodi Phunzilo la Baibulo Limacitika Bwanji? na kukambilana (koma musawatambitse)
Ulendo Wobwelelako: (4 mineti kapena kucepelapo) bhs—Chulani ndi kukambilana za vidiyo (koma musawatambitse) yakuti Kodi Phunzilo la Baibulo Limacitika Bwanji? pokambilana ndi amene mumapelekela magazini.
Phunzilo la Baibo: (6 mineti kapena kucepelapo) bhs peji 217
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Tizionetsa Ulemu Tikafika pa Khomo la Munthu”: (15 min.) Nkhani yokambilana ya woyang’anila nchito. Yambani ndi kutambitsa vidiyo ya malangizo a mmene tingaonetsele ulemu tikafika pakhomo la munthu.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) kr nkhani 15 mapa. 18-28
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 29 na Pemphelo