CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | EZEKIELI 21-23
Ufumuwo ni wa Uyo Ali Woyenelela Mwalamulo
Yopulinta
Yesu ndiye anali “woyenelela mwalamulo” kulandila ufumu pokwanilitsa ulosi wa Ezekieli.
Gen. 49:10
Kodi Mesiya anacokela m’fuko la ndani?
2 Sam. 7:12, 16
Ni ufumu wa ndani umene udzakhalapo kosatha?
Kodi Mateyu anafotokoza kuti mzela wobadwila wa Yesu ni wopitila mwa ndani?