August 14-20
EZEKIELI 32-34
Nyimbo 144 na Pemphelo
Mau Oyamba (3 mineti kapena kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU
“Udindo Waukulu wa Mlonda”: (10 min.)
Ezek. 33:7—Yehova anaika Ezekieli kukhala mlonda (it-2 peji 1172 pala. 2)
Ezek. 33:8, 9—Mlonda anali kupewa mlandu wa magazi mwa kucenjeza anthu (w88-E 1/1 peji 28 pala. 13)
Ezek. 33:11, 14-16—Yehova adzapulumutsa aja amene amamvela cenjezo (w12 3/15 peji 15 pala. 3)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Ezek. 33:32, 33—N’cifukwa ciani tifunika kulimbikilabe kulalikila olo kuti anthu akhale ndi mphwayi [kupanda cidwi]? (w91 3/15 peji 17 pala. 16-17)
Ezek. 34:23—Kodi lembali lakwanilitsika bwanji? (w07 4/1 peji 26 pala. 3)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 mineti kapena kucepelapo) Ezek. 32:1-16
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (2 mineti kapena kucepelapo) g17.4 nkhani ya pacikuto—Yalani maziko a ulendo wobwelelako.
Ulendo Wobwelelako: (4 mineti kapena kucepelapo) g17.4 nkhani ya pacikuto—Itanilani munthuyo kumisonkhano.
Phunzilo la Baibo: (6 min. kapena kucepelapo) fg phunzilo 2 mapa. 9-10—Onetsani mmene tingam’fikile pamtima wophunzila.
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Kulitsani Makhalidwe Aumulungu—Kulimba Mtima: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Muzipewa Zinthu Zimene Zingakulepheletseni Kukhala Wokhulupilika—Kuopa Anthu.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) kr nkhani 16 mapa. 6-17
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 117 na Pemphelo