LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb17 September tsa. 6
  • September 25–October 1

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • September 25–October 1
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano —2017
mwb17 September tsa. 6

September 25–October 1

DANIELI 4-6

  • Nyimbo 67 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 mineti kapena kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Kodi Mukutumikila Yehova Mosalekeza?”: (10 min.)

    • Dan. 6:7-10—Danieli anaika moyo wake paciswe pofuna kutumikila Yehova mosalekeza (w10 11/15 peji 6 pala. 16; w06 11/1 peji 24 pala. 12

    • Dan. 6:16, 20—Mfumu Dariyo inaona kuti Danieli anali paubwenzi wolimba na Yehova (w03 9/15 peji 15 pala. 2

    • Dan. 6:22, 23—Yehova anadalitsa Danieli cifukwa cosagwedezeka pakumulambila (w10 2/15 peji 18 pala. 15)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Dan. 4:10, 11, 20-22—Kodi mtengo waukulu umene Nebukadinezara analota umaimila ciani? (w07 9/1 peji 18 pala. 5)

    • Dan. 5:17, 29—N’cifukwa ciani poyamba Danieli anakana mphatso zocokela kwa Mfumu Belisazara, koma pambuyo pake analandila? (w88 10/1 peji 30 mapa. 3-5; dp peji 109 pala. 22)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 mineti kapena kucepelapo) Dan. 4: 29-37

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 mineti kapena kucepelapo) inv

  • Ulendo Wobwelelako: (4 mineti kapena kucepelapo) inv—Citani ulendo wobwelelako mwa kuseŵenzetsa kapepa ka ciitano kamene kanagaŵilidwa pa ulendo woyamba.

  • Phunzilo la Baibo: (6 mineti kapena kucepelapo) bhs peji 129 pala. 16—Limbikitsani wophunzila kukhalabe wokhulupilika pamene akutsutsidwa ndi a m’banja lake.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 139

  • “Aphunzitseni Kutumikila Yehova Mosalekeza”: (15 min.) Kukambilana. Ndiyeno tambitsani na kukambilana vidiyo yoonetsa wofalitsa waluso akulalikila pamodzi na wofalitsa watsopano.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) kr nkhani 18 mapa. 9-20, bokosi “Kodi Zopeleka Zathu Zimagwila Nchito Yanji?,” na kabokosi kobwelelamo “Kodi Mumaona Kuti Ufumu wa Mulungu ndi Weniweni?”

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 73 na pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani