LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 September tsa. 3
  • September 10-16

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • September 10-16
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 September tsa. 3

September 10-16

YOHANE 3-4

  • Nyimbo 57 na Pemphelo

  • Mau Oyamba (3 min. olo kucepelapo)

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU

  • “Yesu Alalikila Mayi Wacisamariya”: (10 min.)

    • Yoh. 4:6, 7—Ngakhale kuti anali atalema, Yesu anatengelapobe mwayi n’kukambilana na mayi wacisamariya (“atatopa” nwtsty mfundo younikila pa Yoh. 4:6)

    • Yoh. 4:21-24—Makambilano oceza a Yesu pothela pake anakhala ulaliki kwa anthu ambili

    • Yoh. 4:39-41—Cifukwa ca khama la Yesu, Asamariya ambili anakhulupilila mwa iye

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)

    • Yoh. 3:29—Kodi vesiyi itanthauza ciani? (“mnzake wa mkwati” nwtsty mfundo younikila)

    • Yoh. 4:10—Pamene Yesu anachula za “madzi amoyo,” kodi mwina mzimayi wacisamaliya anaganiza za ciani? Koma kodi Yesu anatanthauzanji? (“madzi amoyo,” nwtsty mfundo younikila)

    • Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?

    • Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Yoh. 4:1-15

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo.

  • Vidiyo ya Kubwelelako Koyamba: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Nkhani: (6 min. olo kucepelapo) wp16.2 peji 9 mapa. 1-4—Mutu: Kutanthauzila Lemba la Yohane 4:23.

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 77

  • “Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kuyambitsa Makambilano Otsogolela ku Ulaliki”: (15 min.) Kukambilana. Tsilizani mwa kulimbikitsa onse kuti mkati mwa wiki ayeseko kuyambitsa makambilano, olo amodzi cabe. Pa msonkhano wotsatila wa mkati mwa wiki, ofalitsa akafotokoze mmene zinayendela.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 35 mapa. 20-27, na bokosi “Ankabwereza Mfundo Pophunzitsa” pa peji 89

  • Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)

  • Nyimbo 35 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani