LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb18 September tsa. 4
  • Tsatilani Yesu na Colinga Cabwino

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Tsatilani Yesu na Colinga Cabwino
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Nkhani Zofanana
  • Olungama Palibe Cowakhumudwitsa
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2021
  • Kodi Mudzapunthwa Cifukwa ca Yesu?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2021
  • Muzisamala Kuti Musadzipunthwitse Kapena Kupunthwitsa Ena
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • Kodi Muli na Maganizo a Ndani?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
mwb18 September tsa. 4

CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU | YOHANE 5-6

Tsatilani Yesu na Colinga Cabwino

6:9-11, 25-27, 54, 66-69

Yesu atapeleka fanizo limene ophunzila ake analephela kulimvetsetsa, ena anakhumudwa ndipo analeka kumutsatila. Apo n’kuti Yesu atawapatsa cakudya anthuwo mozizwitsa, poonetsa kuti mphamvu zake zinali zocokela kwa Mulungu. Kodi iwo anakhumudwa cifukwa ciani? Cifukwa cakuti anali kutsatila Yesu na zolinga zadyela. Anali kungofunako zabwino zakuthupi.

Na ise tiyenela kudzifunsa kuti: Kodi nimatsatila Yesu pa colinga canji? Kodi cacikulu ni maubwino amene nimapezapo pali pano, na madalitso amene nidzalandila m’tsogolo? Kapena n’cifukwa cakuti nimakonda Yehova, na kucita zinthu zom’kondweletsa?

N’cifukwa ciani tingadzigwilitse mwala ngati zolinga zathu zazikulu potumikilaYehova ni izi?

Yesu adyetsa ophunzila ake mozizwitsa; ophunzila ambili a Yesu aleka kumutsatila, ndipo Yesu afunsa atumwi ake ngati nawonso afuna kuleka kumutsatila
  • Kukonda kukhala pamodzi na anthu a Mulungu

  • Kufuna kudzakhala m’Paradaiso

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani