LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 March tsa. 6
  • March 30–April 5

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • March 30–April 5
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 March tsa. 6

March 30–April 5

GENESIS 29-30

  • Nyimbo 93 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yakobo Akwatila”: (10 min.)

    • Gen. 29:18-20—Yakobo anavomela kuseŵenzela Labani zaka 7 kuti akwatile Rakele (w03 10/15 29 ¶6)

    • Gen. 29:21-26—Labani anapusitsa Yakobo pom’patsa Leya m’malo mwa Rakele (w07 10/1 8-9; it-2 341 ¶3)

    • Gen. 29:27, 28—Ngakhale kuti Yakobo anakumana na zovuta, anayesetsa kucita zinthu moyenela

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)

    • Gen. 30:3​—N’cifukwa ciani Rakele anakamba kuti ana amene Biliha anabeleka kwa Yakobo ni ake? (it-1 50)

    • Gen. 30:14, 15—N’cifukwa ciani Rakele ayenela kuti anataya mwayi wokhala na pakati mwa kuusinthanitsa na mandereki? (w04 1/15 28 ¶7)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova Mulungu, ulaliki, kapena mbali ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Gen. 30:1-21 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Citani khama pa kuŵelenga na kuphunzitsa (10 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Khalani Wolimbikitsa Komanso Wotsitsimula, ndiyeno kambilanani phunzilo 16 m’bulosha ya Kuphunzitsa.

  • Phunzilo la Baibo: (5 min. olo kucepelapo) bhs 59 ¶21-22 (th phunzilo 18)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 57

  • • “Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kulalikila Anthu Akhungu”: (10 min.) Nkhani yokambilana yokambidwa na woyang’anila utumiki. Funsani omvetsela mafunso aya: N’cifukwa ciani tifunika kuganizila zosoŵa za anthu osaona? N’kuti kumene tingapeze anthu akhungu? Kodi tingawafikile bwanji? Ni zida ziti zimene tili nazo zothandiza anthu osaona kupita patsogolo mwauzimu?

  • Zimene Gulu Likukwanilitsa: (5 min.) Tambitsani vidiyo yakuti Zimene Gulu Likukwanilitsa ya March.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 110

  • Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)

  • Nyimbo 30 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani