LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 March tsa. 6
  • Yakobo Akwatila

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yakobo Akwatila
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • Nkhani Zofanana
  • Yakobo Ali Ndi Banja Lalikulu
    Buku Langa La Nkhani Za M’baibo
  • Yakobo Ayenda Ku Harana
    Buku Langa La Nkhani Za M’baibo
  • Yakobo na Esau Akhalanso Pamtendele
    Maphunzilo Amene Tingatengemo m’Baibo
  • Yakobo Analandila Madalitso Omuyenelela
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 March tsa. 6

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 29-30

Yakobo Akwatila

29:18-28

Mwamuna na mkazi wake akukambilana, agwilana manja, ndipo akhala moyandikana. Pambali pawo pali Baibo yotsegula.

Yakobo sanadziŵe mavuto amene anali kudzakumana nawo m’cikwati. Rakele na Leya, anadana koopsa. (Gen. 29:32; 30:1, 8) Koma ngakhale kuti anakumana na mavuto, Yakobo anaona kuti Yehova anali naye. (Gen. 30:29, 30, 43) Ndipo m’kupita kwa nthawi, mbadwa zake zinakhala mtundu wa Isiraeli.—Rute 4:11.

Masiku anonso, anthu amene amasankha kuloŵa m’banja amakumana na mavuto. (1 Akor. 7:28) Ngakhale n’conco, iwo amakhala na mabanja abwino komanso acimwemwe cifukwa codalila Yehova na kuseŵenzetsa mfundo za m’Baibo.—Miy. 3:5, 6; Aef. 5:33.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani