LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 March tsa. 5
  • Yakobo Analandila Madalitso Omuyenelela

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yakobo Analandila Madalitso Omuyenelela
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • Nkhani Zofanana
  • Yakobo na Esau Akhalanso Pamtendele
    Maphunzilo Amene Tingatengemo m’Baibo
  • Ana Amapasa Osiyana
    Buku Langa La Nkhani Za M’baibo
  • Yakobo Analandila Coloŵa
    Maphunzilo Amene Tingatengemo m’Baibo
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 March tsa. 5
Yakobo wavala covala ca Esau komanso waika ubweya wa mbuzi m’khosi na mu mkono mwake, ndiyeno Isaki akugwila mkono wa Yakobo.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 27-28

Yakobo Analandila Madalitso Omuyenelela

27:6-10, 18, 19, 27-29

Kudalitsa Yakobo kwa Isaki kunakwanilitsa ulosi.

  • Mapu ya Dziko Lolonjezedwa, yoonetsa nthaka ya Aisiraeli yaconde komanso yobiliŵila poiyelekezela na nthaka youma ya Aedomu.

    27:28—Yehova anapatsa mbadwa za Abulahamu dziko laconde, “loyenda mkaka ndi uci.”—Deut. 26:15

  • 27:29—Aisiraeli (mbadwa za Yakobo) anakhala amphamvu kuposa Aedomu (mbadwa za Esau).—Gen. 25:23; 2 Sam. 8:14

  • 27:29—Cifukwa ca cidani cawo pa Aisiraeli, Aedomu anatembeleledwa ndipo m’kupita kwa nthawi, mtundu wawo unawonongedwa.—Ezek. 25:12-14

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani