LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 November tsa. 5
  • Njila Yoonetsela Kuyamikila

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Njila Yoonetsela Kuyamikila
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • Nkhani Zofanana
  • N’cifukwa Ciani Tiyenela Kuonetsa Kuyamikila?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2019
  • Mfundo Zimene Tingaphunzile mu Buku la Levitiko
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2019
  • Pitilizani Kufuna-funa Ufumu Coyamba
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2018
  • “Musamade Nkhawa ndi Kanthu Kalikonse”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 November tsa. 5
Banja laciisiraeli likudya nyama imene yapelekedwa monga nsembe yaciyanjano.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LEVITIKO 6–7

Njila Yoonetsela Kuyamikila

7:11-15, 20

Nsembe zaciyanjano zimene Aisiraeli anali kupeleka zimatikumbutsa kufunika koyamikila Yehova m’mapemphelo athu komanso mwa khalidwe lathu.—Afil. 4:6, 7; Akol. 3:15.

  • Popemphela, kodi tingamuyamikile Yehova pa zinthu ziti?—1 Ates. 5:17, 18

  • Kodi kuonetsa kuyamikila kumatipindulitsa bwanji?

  • Kodi zingatheke bwanji munthu kudya “pathebulo la ziwanda”? Nanga kucita zimenezi kungaonetse bwanji kuti sitiyamikila kwa Yehova?—1 Akor. 10:20, 21

Mayi waciisiraeli akuyang’ana kumwamba na kuyamika Yehova.
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani