LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb20 November tsa. 6
  • November 30–December 6

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • November 30–December 6
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
mwb20 November tsa. 6

November 30–December 6

LEVITIKO 8-9

  • Nyimbo 16 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (1 min.)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Umboni wa Dalitso la Yehova”: (10 min.)

    • Lev. 8:6-9, 12—Mose analonga ansembe (it-1 1207)

    • Lev. 9:1-5—Mtundu wa Aisiraeli unalipo pamene ansembewo anapeleka nsembe zanyama kwa nthawi yoyamba (it-1 1208 ¶8)

    • Lev. 9:23, 24—Yehova anaonetsa kuti anawavomeleza ansembewo (w19.11 23 ¶13)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (10 min.)

    • Lev. 8:6—Mulungu anali kufuna kuti ansembe azikhala oyela. Kodi tiphunzilapo ciani pamenepa? (w14 11/15 9 ¶6)

    • Lev. 8:14-17—Pa nthawi yolonga ansembe, n’cifukwa ciani Mose ndiye anapeleka nsembe osati Aroni? (it-2 437 ¶3)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Lev. 8:31–9:7 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (3 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno muonetseni mwininyumba mfundo inayake ya m’magazini yogaŵila ya Nsanja ya Mlonda ya Na. 2 2020, na kum’gaŵila magaziniyo. (th phunzilo 6)

  • Ulendo Wobwelelako: (4 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno m’fotokozeleni za webusaiti yathu mwininyumba, na kumusiila kakhadi kongenela pa jw.org. (th phunzilo 4)

  • Phunzilo la Baibo: (5 min. olo kucepelapo) bhs 84 ¶6-7 (th phunzilo 11)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 58

  • “Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kulalikila Pafoni”: (15 min.) Nkhani yokambilana yokambidwa na woyang’anila utumiki. Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min. olo kucepelapo) lfb phunzilo 5, 6

  • Mawu Othela (3 min. olo kucepelapo)

  • Nyimbo 150 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani