LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 January tsa. 15
  • February 22-28

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • February 22-28
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 January tsa. 15

February 22-28

NUMERI 5–6

  • Nyimbo 81 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1.)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Kodi Mungatengele Bwanji Citsanzo ca Anazili?”: (Mph. 10.)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu (Mph. 10.)

    • Num. 6:6, 7—Kodi zinatheka bwanji kuti Samisoni agwile mitembo ya anthu amene anafa koma n’kupitilizabe kukhala Mnazili? (w05 1/15 30 ¶2)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4.) Num. 5:1-18 (th phunzilo 10)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3.) Yambani na makambilano acitsanzo. Ndiyeno chulani na kukambilana vidiyo yakuti Mboni za Yehova—Kodi Ndife Anthu Otani? (koma musaitambitse) (th phunzilo 1)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4.) Yambani na makambilano acitsanzo. Gaŵilani cofalitsa ca mu Thuboksi yathu. (th phunzilo 3)

  • Nkhani: (Mph. 5.) w06 1/15 32—Mutu: Zinthu Zocititsa Cidwi Zimene Anapeza Zoonetsa Kuti Baibo Ni Yolondola Pofotokoza Mbili Yakale. (th phunzilo 13)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 76

  • “Kodi Mudzacitako Upainiya Wothandiza m’Mwenzi wa March Kapena April?”: (Mph. 5.) Kukambilana.

  • Kampeni Yomemeza Anthu ku Cikumbutso Idzayamba pa Ciŵelu, February 27: (Mph. 10.) Kukambilana. Gaŵilani aliyense m’gulu kapepa koitanila anthu ku Cikumbutso, na kukambilana mwacidule zimene zilimo. Fotokozani makonzedwe a pampingo panu a mokafolela magawo. Tambitsani vidiyo ya ulaliki wacitsanzo. Ndiyeno funsani omvetsela mafunso awa: Ni pa nthawi iti pamene tiyenela kutambitsa vidiyo yakuti Kukumbukila Imfa ya Yesu? Kodi mwininyumba angaonetse cidwi m’njila zina ziti?

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30.) lfb phunzilo 23, 24

  • Mawu Othela (Mph. 3.)

  • Nyimbo 49 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani