January Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano January-February 2021 January 4-10 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Khalanibe na Khalidwe Loyela UMOYO WATHU WACIKHRISTU Makolo, Phunzitsani Ana Anu Zimene Afunika Kudziŵa January 11-17 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Yehova Amapatula Anthu Ake UMOYO WATHU WACIKHRISTU Tetezani Cikwati Canu January 18-24 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Zikondwelelo Zapacaka Zokhala na Tanthauzo kwa Ife UMOYO WATHU WACIKHRISTU Misonkhano Ikulu-ikulu Yapacaka Imatipatsa Mwayi Woonetsana Cikondi January 25-31 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Caka ca Ufulu Komanso Ufulu Wam’tsogolo UMOYO WATHU WACIKHRISTU Tidzapeza Ufulu M’tsogolo mwa Thandizo la Mulungu na Khristu February 1-7 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Zimene Tingacite Kuti Tilandile Madalitso a Yehova UMOYO WATHU WACIKHRISTU Sankhani Kutumikila Yehova February 8-14 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Yehova Alinganiza Anthu Ake Mwadongosolo UMOYO WATHU WACIKHRISTU Gulu Limene Limalalikila Aliyense February 15-21 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Utumiki wa Alevi February 22-28 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kodi Mungatengele Bwanji Citsanzo ca Anazili? UMOYO WATHU WACIKHRISTU Kodi Mudzacitako Upainiya Wothandiza m’Mwezi wa March Kapena April? CITANI KHAMA PA ULALIKI Makambilano Acitsanzo