LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 January tsa. 12
  • Yehova Alinganiza Anthu Ake Mwadongosolo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yehova Alinganiza Anthu Ake Mwadongosolo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Kodi Zocita za Munthu Mmodzi Zingapindulitse Ambili?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Mmene Yehova Amatsogolela Anthu Ake
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Kodi Mumaphunzilapo Kanthu pa Zolakwa Zanu?
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 January tsa. 12

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Alinganiza Anthu Ake Mwadongosolo

[Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Numeri.]

Aisiraeli anamanga misasa yawo m’magulu a mafuko atatu-atatu (Num. 1:52, 53; w94 12/1 9 ¶4)

Aisiraeli ayenela kuti analipo 3,000,000 kapena kuposelapo (Num. 2:32, 33; it-1 397 ¶4)

Yehova amafuna kuti anthu ake azimulambila mwadongosolo. Umu ni mmene zinalili na mtundu wa Aisiraeli, ndipo ni mmenenso zilili kwa ife masiku ano. —1 Akor. 14:33, 40.

Cithunzi coonetsa mmene Aisiraeli anali kumangila misasa yawo. Cihema copatulika cili pakati. Pafupi kwambili na cihema copatulikaco pali misasa ya mabanja a fuko la Levi: Banja la Aroni kum’maŵa, Akohati kum’mwela, Agerisoni kumadzulo, ndiponso Amerari kumpoto. Mafuko 12 a Isiraeli ali kutali na cihema copatulikaco. Kum’maŵa kuli mafuko a Isakara, Yuda, na Zebuloni. Kum’mwela kuli mafuko a Gadi, Rubeni, na Simiyoni. Kumadzulo kuli mafuko a Benjamini, Efuraimu, na Manase. Kumpoto kuli mafuko a Nafitali, Dani, na Aseri.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi ningaonetse bwanji kuti nikucilikiza makonzedwe a Yehova na mtima wonse?’

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani