LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 January tsa. 12
  • February 8-14

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • February 8-14
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 January tsa. 12

February 8-14

NUMERI 1-2

  • Nyimbo 123 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1.)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova Alinganiza Anthu Ake Mwadongosolo”: (Mph. 10.)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 10.)

    • Num. 1:2, 3—N’cifukwa ciani Aisiraeli anali kulembedwa m’kaundula? (it-2 764)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4.) Num. 1:1-19 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3.) Yambani na makambilano acitsanzo. Pemphani mwininyumba kuti muziphunzila naye Baibo. Ndiyeno, chulani na kukambilana vidiyo yakuti Kodi Phunzilo la Baibulo Limacitika Bwanji? (koma musaitambitse). (th phunzilo 9)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4.) Yambani na makambilano acitsanzo. Sinthankoni ulaliki wanu kuti ugwilizane na nkhawa za mwininyumba, kenako ŵelengani lemba loyenelela. (th phunzilo 12)

  • Nkhani: (Mph. 5.) w08 7/1 21—Mutu: N’cifukwa Ciani Nthawi Zambili Baibo Imangochula Mafuko 12 a Isiraeli Pamene M’ceni-ceni Anali Mafuko 13? (th phunzilo 7)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 57

  • “Gulu Limene Limalalikila Aliyense”: (Mph. 10.) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Khala Bwenzi la Yehova—Kulalikila m’Citundu Cina. Kambilanani na omvetsela mbali zina za pa JW Language® app.

  • Zofunikila za Mpingo: (Mph. 5.)

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30.) lfb phunzilo 20, 21

  • Mawu Othela (Mph. 3.)

  • Nyimbo 148 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani