LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • th phunzilo 9 tsa. 12
  • Kuseŵenzetsa Bwino Zitsanzo Zooneka

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kuseŵenzetsa Bwino Zitsanzo Zooneka
  • Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa
  • Nkhani Zofanana
  • Seŵenzetsani Mavidiyo Pophunzitsa Anthu Baibo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2019
  • Phunzilani Zambili pa Zithunzi
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2025
  • Kunola Luso Lathu mu Ulaliki—Kuseŵenzetsa Mavidiyo Pophunzitsa
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
  • Yesetsani Kuwafika pa Mtima Omvela
    Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa
Citani Khama pa Kuŵelenga na Kuphunzitsa
th phunzilo 9 tsa. 12

PHUNZILO 9

Kuseŵenzetsa Bwino Zitsanzo Zooneka

Lemba losagwila mawu

Genesis 15:5

ZOFUNIKILA: Kuti mumveketse bwino mfundo zofunika mungaseŵenzetse zitsanzo za zinthu zooneka.

MOCITILA:

  • Sankhani zinthu zooneka zothandizila kuphunzitsa. Mungaseŵenzetse mapikica, zithunzi, mapu, chati ya nthawi, na zinthu zina zooneka, kotelo kuti mumveketse mfundo zofunika, osati tumfundo tung’ono-tung’ono. Onetsetsani kuti omvela anu asakumbukile citsanzo cooneka cokhaco, koma maka-maka phunzilo lake.

  • Tsimikizani kuti omvela anu akutha kuciona bwino citsanzo coonekaco.

    Tumalangizo tothandiza

    Pasadakhale, pezelantuni zinthu zilizonse zimene mufuna kukaseŵenzetsa monga zitsanzo zooneka.

MU ULALIKI

Onetsani womvela wanu pikica kapena cithunzi cili m’cofalitsa, na kum’pempha kuti akambepo. Ngati n’kofunikila, m’funseni mafunso ena owonjezela. Potambitsa vidiyo, muyandikileni kuti aione bwino. Si bwino kumalankhula pamene vidiyo ikutambika.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani