LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 January tsa. 16
  • Kodi Mudzacitako Upainiya Wothandiza m’Mwezi wa March Kapena April?

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kodi Mudzacitako Upainiya Wothandiza m’Mwezi wa March Kapena April?
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Mipata Yoonjezeka Yotamanda Yehova
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2013
  • Kodi Mudzacitako Upainiya Wothandiza?
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2013
  • Pangani Nyengo Ino ya Cikumbutso Kukhala Yosangalatsa
    Utimiki Wathu wa Ufumu—2014
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 January tsa. 16
Kagulu ka ofalitsa kakucoka pa Nyumba ya Ufumu na kasitandi ka ulaliki.

“Cikondi cimene Khristu ali naco cimatikakamiza.”—2 Akor. 5:14

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

Kodi Mudzacitako Upainiya Wothandiza m’Mwezi wa March Kapena April?

Kodi mungakonde kucita zambili mu utumiki wa Yehova pa nyengo ya Cikumbutso? (2 Akor. 5:14, 15) Ofalitsa amene adzacitako upainiya wothandiza m’mwezi wa March na April, adzakhala na ufulu wosankha kulalikila maola 30 kapena 50. Ngati mungakwanitse kutengako mbali pa kampeni yapadela imeneyi, mungasaine fomu na kuipeleka ku Komiti ya Utumiki ya Mpingo. M’miyezi imeneyi, maina a abale na alongo amene adzavomelezedwa kucitako upainiya wothandiza, adzalengezedwa ku mpingo. Izi zidzalimbikitsa mpingo kuti uwacilikize apainiya mu ulaliki. Tiyeni tonse tikatengemo mbali mokwanila mu ulaliki pa nyengo ya Cikumbutso, n’colinga cakuti tikanole maluso athu na kulimbikitsana wina na mnzake.—1 Ates. 5:11.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani