LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 January tsa. 4
  • January 11-17

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • January 11-17
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 January tsa. 4

January 11-17

LEVITIKO 20-21

  • Nyimbo 80 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1.)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Yehova Amapatula Anthu Ake”: (Mph. 10.)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 10.)

    • Lev. 21:5—N’cifukwa ciani Cilamulo ca Mulungu cinaletsa kudzitematema kapena kudzicekaceka? (it-1 563)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4.) Lev. 20:1-13 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5.) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Wobwelelako: Pemphelo—1 Yoh. 5:14. Nthawi iliyonse vidiyo ikaima, na imwe iimitseni na kufunsa omvetsela mafunso amene aonekela pa sikilini.

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3.) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 6)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5.) Yambani na makambilano acitsanzo, ndiyeno gaŵilani bulosha yakuti Uthenga Wabwino, na kuyambitsa phunzilo la Baibo pa phunzilo 12. (th phunzilo 19)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 131

  • “Tetezani Cikwati Canu”: (Mph. 15.) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Tifunika ‘Kuthamanga Mopilila’—Tsatilani Malamulo a Mpikisano.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30.) lfb phunzilo 14, 15

  • Mawu Othela (Mph. 3.)

  • Nyimbo 3 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani