LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 January tsa. 16
  • Makambilano Acitsanzo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Makambilano Acitsanzo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Tumitu
  • Nkhani Zofanana
  • Ulendo Woyamba
  • Ulendo Wobwelelako
  • Kampeni Yomemeza Anthu ku Cikumbutso (February 27–March 27)
  • Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
  • Makambilano Acitsanzo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2020
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 January tsa. 16

CITANI KHAMA PA ULALIKI

Makambilano Acitsanzo

Ulendo Woyamba

Funso: Kodi Mulungu amamvetsela mapemphelo?

Lemba: Sal. 65:2

Ulalo: Ni zinthu ziti zimene tingapemphelele?

PEZANI LEMBALI M’CIDA CA M’THUBOKSI YATHU:

  • ‘Nsanja ya Mlonda’ Na. 1 2021.

    wp21.1 5

Ulendo Wobwelelako

Funso: Ni zinthu ziti zimene tingapemphelele?

Lemba: 1 Yoh. 5:14

Ulalo: Kodi Mulungu amayankha bwanji mapemphelo athu?

PEZANI LEMBALI M’CIDA CA M’THUBOKSI YATHU:

  • ‘Nsanja ya Mlonda’ Na. 1 2021.

    wp21.1 10

Kampeni Yomemeza Anthu ku Cikumbutso (February 27–March 27)

“Tabwela [kapena takutumilani kapenanso takulembelani] na colinga cofuna kukuitanilani ku cocitika capadela ca anthu mamiliyoni ambili. Cocitika cimeneci ni mwambo wokumbukila imfa ya Yesu.” Ndiyeno patsani munthuyo [kapena tumizani pa meseji kapena pa imelo] kapepa ka ciitanilo. “Kapepa ka ciitanilo aka kaonetsa nthawi na malo kumene cocitikaci cidzacitikile kwathu kuno [kapena mmene mungalumikizile ku msonkhanowu pa intaneti]. Tikuitanilaninso ku nkhani yapadela imene idzakambidwa kumapeto kwa mlungu woti cikumbutso cicitika mlungu wotsatila.”

Funso la Ulalo Akaonetsa Cidwi: N’cifukwa ciani Yesu anafa?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani