LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 January tsa. 2
  • January 4-10

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • January 4-10
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 January tsa. 2

January 4-10

LEVITIKO 18–19

  • Nyimbo 122 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1.)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Khalanibe na Khalidwe Loyela”: (Mph. 10.)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu (Mph. 10.)

    • Lev. 19:9, 10—Kodi Cilamulo cinaonetsa bwanji kuti Mulungu amaganizila osauka? (w06 6/15 22 ¶11)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4.) Lev. 18:1-15 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (Mph. 5.) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Ulendo Woyamba: Pemphelo—Sal. 65:2. Nthawi iliyonse vidiyo ikaima, na imwe iimitseni na kufunsa omvetsela mafunso amene aonekela pasikilini.

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3.) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. (th phunzilo 3)

  • Nkhani: (Mph. 5.) w02 2/1 29—Mutu: Kodi Malamulo Oletsa Ukwati wa Pacibale Amene ali M’Cilamulo ca Mose Amagwila Nchito kwa Akhristu Lelolino Pamlingo Wotani? (th phunzilo 7)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 134

  • Khala Bwenzi la Yehova—Tetezani Ana Anu: (Mph. 5.) Nkhani yokambidwa na mkulu. Onetsani vidiyoyi. Ndiyeno fotokozani zimene tiphunzilapo.—Miy. 22:3.

  • “Makolo, Phunzitsani Ana Anu Zimene Afunika Kudziŵa”: (Mph. 10.) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Mangani Nyumba Imene Idzakhalitsa—Tetezani Ana Anu ku “Zinthu Zoipa”.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30.) lfb phunzilo 13

  • Mawu Othela (Mph. 3.)

  • Nyimbo 113 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani