LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 January tsa. 2
  • Khalanibe na Khalidwe Loyela

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Khalanibe na Khalidwe Loyela
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Pitilizani Kuonetsa Kukula kwa Cikondi Canu Pa Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Zikondwelelo Zapacaka Zokhala na Tanthauzo kwa Ife
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Kodi Mukumbukila?
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2019
  • Yehova Amapatula Anthu Ake
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 January tsa. 2
Mwamuna amenenso ni tate akuyang’ana kumbali moipidwa pamene waona zinthu zoipa pa kompyuta yake ndipo akuitseka mwamsanga.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Khalanibe na Khalidwe Loyela

Yehova amafuna kuti tizicita zinthu mosiyana ndi anthu a m’dzikoli (Lev. 18:3; w19.06 28 ¶1)

Yehova amaletsa makhalidwe oipa monga kugonana pacibale, mathanyula, komanso kugonana na nyama (Lev. 18:6, 22, 23; w17.02 20 ¶13)

Yehova adzawononga anthu odetsedwa m’dzikoli (Lev. 18:24, 25; Miy. 2:22; w14 7/1 7 ¶2)

Satana safuna kuti tikaloŵe m’dziko latsopano la Mulungu. Koma mfundo za Yehova zingatiteteze ku msampha uliwonse wa Satana.

Tingaonetse bwanji kwa Yehova kuti timadana na zaciwelewele?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani