LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 September tsa. 8
  • Pitilizani Kuonetsa Kukula kwa Cikondi Canu Pa Yehova

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Pitilizani Kuonetsa Kukula kwa Cikondi Canu Pa Yehova
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Mmene Mungakhalile Bwenzi La Mulungu
    Zimene Baibulo Ingatiphunzitse
  • Tingakhale na Mtima Wosagaŵikana Ngakhale Ndife Opanda Ungwilo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • “Yembekezela Yehova”
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2022
  • Yobu Anakhalabe Wokhulupilika Pamene Anali Kuyesedwa
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 September tsa. 8

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Pitilizani Kuonetsa Kukula kwa Cikondi Canu pa Yehova

[Tambitsani vidiyo yakuti Mfundo Zokhudza Buku la Yobu.]

Satana anakamba kuti Yobu anali kukonda Yehova na kum’tumikila cifukwa ca dyela (Yobu 1:​8-11; w18.02 6 ¶16-17)

Satana amakamba kuti timakonda Yehova cifukwa ca dyela (Yobu 2:​4, 5; w19.02 5 ¶10)

Mlongo amene wavala cisoti codzitetezela, akulalikila mzimayi pambuyo pa tsoka la zacilengedwe.

Yehova wapatsa aliyense wa ife mwayi wotsimikizila mwa zocita zathu kuti Satana ni wabodza. (Miy. 27:11) Tingaonetse kuti timamukonda kwambili Yehova mwa kumuika patsogolo mu umoyo wathu pa nthawi yabwino komanso yovuta.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani