LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb23 November tsa. 10
  • Tingakhale na Mtima Wosagaŵikana Ngakhale Ndife Opanda Ungwilo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Tingakhale na Mtima Wosagaŵikana Ngakhale Ndife Opanda Ungwilo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Nkhani Zofanana
  • Khalanibe na Mtima Wamphumphu!
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2019
  • Pitilizani Kuonetsa Kukula kwa Cikondi Canu Pa Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
  • Yobu Anakhalabe Wokhulupilika Pamene Anali Kuyesedwa
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Msonkhano (2016)
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2023
mwb23 November tsa. 10

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Tingakhale na Mtima Wosagaŵikana Ngakhale Ndife Opanda Ungwilo

Yobu anaimba Mulungu mlandu (Yobu 27:​1, 2)

Yobu anali na mtima wosagaŵikana ngakhale kuti analakwitsapo zinthu zina (Yobu 27:5; it-1 1210 ¶4)

Kukhala na mtima wosagaŵikana kumafuna kumukonda na mtima wonse Yehova, osati kukhala angwilo (Mat. 22:37; w19.02 3 ¶3-5)

M’bale akudziimba mlandu pa zolakwa zake zakale. Pambuyo pake, waleka kudziimba mlandu ndipo waleka kudziimba mlandu.

ZOYENELA KUZISINKHASINKHA: Kodi kudziŵa kuti Yehova satiyembekezela kucita zinthu mwangwilo kumatithandiza bwanji kusalefuka?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani