LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 January tsa. 4
  • Yehova Amapatula Anthu Ake

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yehova Amapatula Anthu Ake
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Zimene Tingacite Kuti Tilandile Madalitso a Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Yehova Anawamenyela Nkhondo Aisiraeli
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Yehova Analigaŵa Mwanzelu Dziko la Kanani
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Tetezani Coloŵa Canu Camtengo Wapatali
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 January tsa. 4

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Amapatula Anthu Ake

Tiyenela kutsatila malamulo onse a Yehova (Lev. 20:22, 23; w04 10/15 11 ¶12)

Yehova analonjeza anthu ake colowa (Lev. 20:24; it-1 1199)

Yehova amafuna kuti kulambila kwa anthu ake kuzikhala koyela (Lev. 20:25, 26; it-1 317 ¶2)

Yehova amadalitsa anthu amene amakhalabe pa ubale wabwino na iye. Kuti iye apitilize kutiyanja, tifunika kupitiliza kukhala olekana na dzikoli komanso kupewa makhalidwe odetsa.

M’bale wa m’Komiti Yokamba ndi a Cipatala akupeleka malifalensi a zacithandizo ca mankhwala kwa dokotala.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Ni njila ziti za cithandizo ca mankhwala zimene niyenela kupewa zomwe Mulungu sakondwela nazo?’

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani