LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 September tsa. 14
  • Tetezani Coloŵa Canu Camtengo Wapatali

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Tetezani Coloŵa Canu Camtengo Wapatali
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Yehova Analigaŵa Mwanzelu Dziko la Kanani
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Yehova Anawamenyela Nkhondo Aisiraeli
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Malangizo Othela a Yoswa kwa Aisiraeli
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Yehova Amapatula Anthu Ake
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 September tsa. 14

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Tetezani Coloŵa Canu Camtengo Wapatali

Kalebe anateteza coloŵa cake mwa kupitikitsa adani amphamvu (Yos. 15:14; it-1 1083 ¶3)

Aisiraeli ena analephela kuteteza coloŵa cawo kwa anthu amene sanali kulambila Yehova (Yos. 16:10; it-1 848)

Yehova anathandiza aja amene anali kufunitsitsa kuteteza coloŵa cawo (Deut. 20:1-4; Yos. 17:17, 18; it-1 402 ¶3)

Yehova wapatsa Akhristu onse coloŵa camtengo wapatali, cimene ni ciyembekezo ca moyo wosatha. Kuti titeteze coloŵa cathu, tiyenela kudzilimbitsa kuti tisagonje ku mayeselo. Tingacite zimenezo mwa kuŵelenga Baibo, kupezeka ku misonkhano, kulalikila, komanso kupemphela.

Tate akucita kulambila kwa pabanja na mkazi wake komanso ana ake.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi coloŵa canga nimaciteteza?’

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani