LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 September tsa. 10
  • Yehova Anawamenyela Nkhondo Aisiraeli

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Yehova Anawamenyela Nkhondo Aisiraeli
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Yehova Analigaŵa Mwanzelu Dziko la Kanani
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Malangizo Othela a Yoswa kwa Aisiraeli
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Tetezani Coloŵa Canu Camtengo Wapatali
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Yehova Amapatula Anthu Ake
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 September tsa. 10
Yoswa ali pakati pa asilikali a Isiraeli akupempha Yehova kuti aimitse dzuŵa.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yehova Anawamenyela Nkhondo Aisiraeli

Mafumu asanu anagwilizana kuti akathile nkhondo mzinda wa Gibeoni komanso Aisiraeli (Yos. 10:5; it-1 50)

Yehova anamenya nkhondo na mafumu amene anagwilizanawo (Yos. 10:10, 11; it-1 1020)

Yehova anacititsa dzuŵa kuima (Yos. 10:12-14; w04 12/1 11 ¶1)

M’bale akumwetulila ali m’citolokosi.

Tikakumana na cizunzo, timadalila Yehova kuti atithandize kukhalabe okhulupilika. Tidziŵa kuti mwa thandizo lake, palibe boma la anthu limene lingatiletse kum’lambila.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani