LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 January tsa. 6
  • January 18-24

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • January 18-24
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 January tsa. 6

January 18-24

LEVITIKO 22–23

  • Nyimbo 86 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1.)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Zikondwelelo Zapacaka Zokhala na Tanthauzo kwa Ife”: (Mph. 10.)

  • Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (Mph. 10.)

    • Lev. 22:21, 22—N’cifukwa ciani tifunika kukhala okhulupilika na mtima wonse kwa Yehova? (w19.02 3 ¶3)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4.) Lev. 23:9-25 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Ulendo Woyamba: (Mph. 3.) Yambani na makambilano acitsanzo. Gaŵilani magazini imene ikamba zogwilizana na nkhani imene mwininyumba wafunsa. (th phunzilo 13)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4.) Yambani na makambilano acitsanzo. Gaŵilani cofalitsa ca mu Thuboksi yathu. (th phunzilo 9)

  • Nkhani: (Mph. 5.) w07 7/15 26—Mutu: Kodi Ndani Anali Kukolola Balele Woyamba Kuca N’kupita Naye Kukacisi? (th phunzilo 13)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 87

  • “Misonkhano Ikulu-ikulu Yapacaka Imatipatsa Mwayi Woonetsana Cikondi”: (Mph. 15.) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Msonkhano wa Maiko Wakuti “Cikondi Sicitha”!.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30.) lfb phunzilo 16

  • Mawu Othela (Mph. 3.)

  • Nyimbo 128 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani