LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 January tsa. 6
  • Zikondwelelo Zapacaka Zokhala na Tanthauzo kwa Ife

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Zikondwelelo Zapacaka Zokhala na Tanthauzo kwa Ife
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 January tsa. 6
Zithunzi: 1. Banja laciisiraeli likumanga msasa mwacimwemwe pamtenje wa nyumba. 2. Abale akulonjelana mwa kupatsana moni wakumanja pa msonkhano wa mpingo.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Zikondwelelo Zapacaka Zokhala na Tanthauzo kwa Ife

Pasika komanso Cikondwelelo ca Mikate Yopanda Cofufumitsa (Lev. 23:5, 6; it-1 826-827)

Cikondwelelo ca Masabata (Pentekosite) (Lev. 23:15, 16; it-2 598 ¶2)

Cikondwelelo ca Misasa (Lev. 23:34; w14 5/1 25 ¶11)

Tingakhale acimwemwe ngati tiganizila tanthauzo la zikondwelelo zakale za Ayuda komanso mmene Yehova adzakwanilitsila malonjezo ake.—Deut. 16:15.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani