LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 January tsa. 8
  • Caka ca Ufulu Komanso Ufulu Wam’tsogolo

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Caka ca Ufulu Komanso Ufulu Wam’tsogolo
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Yehova Wakonza Zakuti Akupatseni Ufulu
    Nsanja ya Mlonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzila)—2019
  • Yehova Amapatula Anthu Ake
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Yehova Analigaŵa Mwanzelu Dziko la Kanani
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Zimene Tingacite Kuti Tilandile Madalitso a Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 January tsa. 8

Akapolo aciisiraeli akubwelela ku banja lawo na kumalo awo m’Caka ca Ufulu

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Caka ca Ufulu Komanso Ufulu Wam’tsogolo

Caka ca ufulu cinali kuthandiza Aisiraeli kuti asakhale na nkhongole yosatha komanso umphawi wosatha (Lev. 25:10; it-1 871; onani cithunzi pacikuto)

Kugulitsa malo kunali monga kucititsa lendi cabe, ndipo mtengo wake unali kutengela pa phindu limene wogulayo adzapeza pa zokolola za pa malopo (Lev. 25:15; it-1 1200 ¶2)

Yehova anali kuwadalitsa anthu ake akamvela lamulo lokhudza Caka ca Ufulu (Lev. 25:18-22; it-2 122-123)

Posacedwa, anthu okhulupilika adzasangalala mokwanila na madalitso m’Caka ca Ufulu cophiphilitsila pamene adzamasulidwa kothelatu ku ucimo na imfa.—Aroma 8:21.

Zithunzi: Anthu akukonza dziko lapansi kukhala paradaiso. 1. Akuyeletsa mwa kucotsa zinyalala na zinthu zowonongeka. 2. Akumanga nyumba na kukonza tunjila toyendamo. 3. Akusamalila minda.

Kodi aliyense wa ife ayenela kucita ciani kuti akapeze ufulu umene Yehova anatilonjeza?

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani