LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsa. 4
  • March 15-21

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • March 15-21
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 March tsa. 4

March 15-21

NUMERI 11-12

  • Nyimbo 46 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “N’cifukwa Ciani Tiyenela Kupewa Mzimu Wodandaula?”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Num. 11:7, 8—Kodi maonekedwe na makomedwe a mana zinaonetsa bwanji ubwino wa Yehova? (it-2 309)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Num. 11:1-15 (th phunzilo 2)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Kuitanila Anthu ku Cikumbutso: (Mph. 3) Yambani na makambilano acitsanzo. Mwininyumba akaonetsa cidwi, chulani na kukambilana vidiyo yakuti Kukumbukila Imfa ya Yesu (koma musaitambitse). (th phunzilo 11)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Citani ulendo wobwelelako kwa munthu amene anaonetsa cidwi ndipo analandila ciitanilo ca ku Cikumbutso. (th phunzilo 4)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 5) Pambuyo pa nkhani ya Cikumbutso, yambitsani makambilano na munthu wacidwi amene wapezeka pa Cikumbutso, ndipo yankhani funso limene wafunsa lokhudza pulogilamuyo. (th phunzilo 2)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 19

  • “Kodi Mukukonzekela Cikumbutso?”: (Mph. 15) Kukambilana. Pelekani zilengezo zilizonse zofunikila zokhudza makonzedwe a Cikumbutso. Onetsani vidiyo yakuti Mmene Mungapangile Mkate wa Cikumbutso.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 27

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 123 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani