March Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano, March-April 2021 March 1-7 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Zimene Tingaphunzile pa Dongosolo la Msasa wa Aisiraeli March 8-14 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Mmene Yehova Amatsogolela Anthu Ake March 15-21 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU N’cifukwa Ciani Tiyenela Kupewa Mzimu Wodandaula? UMOYO WACIKHILISITU Kodi Mukukonzekela Cikumbutso? March 22-28 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Mmene Cikhulupililo Cimatithandizila Kukhala Olimba Mtima CITANI KHAMA PA ULALIKI | WONJEZELANI CIMWEMWE CANU MU ULALIKI Funsani Mafunso March 29–April 4 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Samalani na Kunyada Komanso Kudzidalila UMOYO WATHU WACIKHRISTU Pewani Kutengela Anthu Osakhulupilika April 5-11 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU “Ine Ndine . . . Colowa Cako” April 12-18 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Khalanibe Ofatsa Mukapanikizika na Mayeso April 19-25 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Yehova Anasintha Tembelelo Kukhala Dalitso CITANI KHAMA PA ULALIKI | WONJEZELANI CIMWEMWE CANU MU ULALIKI Seŵenzetsani Mawu a Mulungu UMOYO WATHU WACIKHRISTU Yehova Amasintha Cizunzo Kukhala Njila Yocitila Umboni April 26–May 2 CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU Kodi Zocita za Munthu Mmodzi Zingapindulitse Ambili? UMOYO WATHU WACIKHRISTU Sankhani Mabwenzi Mwanzelu CITANI KHAMA PA ULALIKI Makambilano Acitsanzo