LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsa. 3
  • March 8-14

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • March 8-14
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 March tsa. 3

March 8-14

NUMERI 9-10

  • Nyimbo 31 na Pemphelo

  • Mawu Oyamba (Mph. 1)

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

  • “Mmene Yehova Amatsogolela Anthu Ake”: (Mph. 10)

  • Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)

    • Num. 9:13—Kodi Akhristu angaphunzilepo ciani pa lamulo limeneli lomwe Aisiraeli anapatsidwa? (it-1 199 ¶3)

    • Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?

  • Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Num. 10:17-36 (th phunzilo 5)

CITANI KHAMA PA ULALIKI

  • Kuitanila Anthu ku Cikumbutso: (Mph. 3) Yambani na makambilano acitsanzo. Mwininyumba akaonetsa cidwi, chulani na kukambilana vidiyo yakuti Kukumbukila Imfa ya Yesu (koma musaitambitse). (th phunzilo 11)

  • Ulendo Wobwelelako: (Mph. 3) Itanilani ku Cikumbutso mnzanu wa kunchito kapena wa kusukulu amene munamulalikilapo kale. (th phunzilo 2)

  • Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) bhs 214, zakumapeto 16 —Itanilani wophunzila wanu ku Cikumbutso, ndipo gwilitsilani nchito Baibo pomufotokozela cifukwa cake sayenela kudyako ziphiphilitso. (th phunzilo 17)

UMOYO WATHU WACIKHRISTU

  • Nyimbo 84

  • Masinthidwe a pa Beteli Amapititsa Patsogolo Nchito Yolalikila: (Mph. 10) Kukambilana. Onetsani vidiyo imeneyi. Ndiyeno funsani omvetsela mafunso aya: Ni cilengezo cotani cimene cinapelekedwa pa msonkhano wapacaka mu 2015? Nanga anafotokoza zifukwa ziŵili ziti zopangila masinthidwe amenewo? Ni masinthidwe ati amene anapangidwa pa Beteli? Ndipo pakhala mapindu otani? Kodi cilengezo cimeneci cinakhudza bwanji nchito yosamutsa ofesi ya nthambi ku Britain? Kodi masinthidwe amenewa aonetsa bwanji kuti Yehova amatitsogolela?

  • Cifukwa Cake Anapita Kukaceza ku Beteli: (Mph. 5) Onetsani vidiyoyi.

  • Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 26

  • Mawu Othela (Mph. 3)

  • Nyimbo 34 na Pemphelo

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani