LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsa. 3
  • Mmene Yehova Amatsogolela Anthu Ake

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Mmene Yehova Amatsogolela Anthu Ake
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • “Ine Ndine . . . Colowa Cako”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Zimene Tingaphunzile pa Dongosolo la Msasa wa Aisiraeli
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Samalani na Kunyada Komanso Kudzidalila
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • “Mukapitikitse Anthu Onse a m’Dzikolo”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 March tsa. 3
M’bale wa m’Bungwe Lolamulila akucititsa pulogilamu ya JW Broadcasting mu situdiyo.

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mmene Yehova Amatsogolela Anthu Ake

Yehova ndiye anali kusankha kumene anthu ake anayenela kupita na nthawi yonyamuka (Num. 9:17, 18; it-1 398 ¶3)

Anthu mumsasa anafunika kulabadila nthawi yomweyo (Num. 9:21, 22; w11 4/15 4-5)

Yehova anali kuseŵenzetsa anthu opanda ungwilo popeleka malangizo (Num. 10:5-8)

Tikamamvela amene amatitsogolela, timaonetsa kuti timamvela Yehova.

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani