LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb21 March tsa. 10
  • “Ine Ndine . . . Colowa Cako”

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • “Ine Ndine . . . Colowa Cako”
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Nkhani Zofanana
  • Mmene Yehova Amatsogolela Anthu Ake
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Samalani na Kunyada Komanso Kudzidalila
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Pitilizani Kupempha Citsogozo ca Yehova
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Utumiki wa Alevi
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
mwb21 March tsa. 10

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

“Ine Ndine . . . Colowa Cako”

Yehova anapatsa ansembe na Alevi utumiki wapadela kwambili (Num. 18:6, 7)

Fuko la Alevi silinalandile malo aliwonse monga colowa, koma Yehova ndiye anali colowa cawo (Num. 18:20, 24; w11 9/15 13 ¶9)

Mtundu wa Aisiraeli unali kupeleka cakhumi ca zokolola zawo pocilikiza Alevi na ansembe (Num. 18:21, 26, 27; w11 9/15 7 ¶4)

Yehova analonjeza ansembe na Alevi kuti adzawapatsa zosoŵa zawo za kuthupi. Nafenso tiyenela kukhala na cikhulupililo cakuti Yehova adzatisamalila tikakhala odzimana pomutumikila.

Zithunzi: Yehova amapeleka zosoŵa zakuthupi za atumiki ake. 1. Mlongo akuika ndalama mu imvulupu. 2. Imvulupu ili kupansi kwa citseko. 3. Mayi amene alela yekha ana wakumbatila mwana wake wamkazi uku akuona ndalama mu imvulupu.
    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani