LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 January tsa. 4
  • Pitilizani Kupempha Citsogozo ca Yehova

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Pitilizani Kupempha Citsogozo ca Yehova
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • “Ine Ndine . . . Colowa Cako”
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Anacita Zinthu Molimba Mtima, Modzipeleka, Komanso Mokangalika
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Zimene Makolo Angaphunzile kwa Manowa na Mkazi Wake
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Samalani na Kunyada Komanso Kudzidalila
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 January tsa. 4

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Pitilizani Kupempha Citsogozo ca Yehova

Mobweleza-bweleza, Aisiraeli anapempha citsogozo ca Yehova (Ower. 20:17, 18, 23; w11 9/15 32 ¶2)

Pamapeto pake, Aisiraeli anadalila Yehova na mtima wonse kuti awathandize kucotsa citonzo pa dzina lake (Ower. 20:26-28)

Tisaleke kupempha citsogozo ca Yehova komanso kum’dalila na mtima wonse (Ower. 20:35 Luka 11:9; w11 9/15 32 ¶4)

Zithunzi: 1. M’bale akufufuza m’Baibo na m’zofalitsa kuti apeze citsogozo. 2. M’baleyo akukamba na dokotala, ndipo akumuonetsa khadi ya DPA.

DZIFUNSENI KUTI: ‘Nikakumana na mavuto, kodi nimapemphela kwa Yehova mwamsanga? Kodi nimapempha nzelu na citsogozo kwa iye mobweleza-bweleza?’

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani