LAIBULALI YA PA INTANETI ya Watchtower
Watchtower
LAIBULALI YA PA INTANETI
Cinyanja
  • BAIBO
  • ZOFALITSA
  • MISONKHANO
  • mwb22 January tsa. 3
  • Kusamvela Malamulo a Mulungu Kumabweletsa Mavuto

Palibe vidiyo yake.

Pepani, vidiyo yakanga kulila.

  • Kusamvela Malamulo a Mulungu Kumabweletsa Mavuto
  • Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
  • Nkhani Zofanana
  • Yefita Anali Munthu Wauzimu
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Mmene Cilamulo Cinaonetsela Kuti Yehova Amadela Nkhawa Osauka
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Utumiki wa Alevi
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
  • Mfundo Zothandiza Kuweluza Milandu Mwacilungamo
    Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2021
Onaninso Zina
Umoyo na Utumiki Wathu Wacikhristu—Kabuku ka Misonkhano—2022
mwb22 January tsa. 3

CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Kusamvela Malamulo a Mulungu Kumabweletsa Mavuto

Mika anaba ndalama za amayi ake (Ower. 17:1, 2)

Mika anali kulambila mafano, ndipo ananyanyala cihema ca Yehova na ansembe ake (Ower. 17:4, 5, 12; it-2 390-391)

M’kupita kwa nthawi, Mika anatsala wopanda ciliconse (Ower. 18:24-26; it-2 391 ¶2)

Mtsikana amene anali Mboni ali na mwana wakhanda, ndipo akulakalaka umoyo wake wakale pamene anali kutumikila Yehova. Pa thebulo pamene wakhala pali kanthu koikamo tumashiki twa ndudu. Mwamuna woledzela wagona pa mpando wa sofa.

DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi napindula bwanji cifukwa comvela Yehova?’

    Mabuku a m’Cinyanja (2000-2025)
    Tulukani
    Loŵani
    • Cinyanja
    • Gawilani
    • Makonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenela Kutsatila
    • Mfundo Yosunga Cisinsi
    • Kusunga Cinsinsi
    • JW.ORG
    • Loŵani
    Gawilani