CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Mfundo Zothandiza Kuweluza Milandu Mwacilungamo
Khalani opanda tsankho (Deut. 16:18, 19; it-1 343 ¶5)
Fufuzani kuti mudziŵe zoona zeni-zeni (Deut. 17:4-6; it-2 511 ¶7)
Pemphani thandizo pa nkhani zovuta (Deut. 17:8, 9; it-2 685 ¶6)
Akulu ayenela kutsatila mosamala mfundo zimenezi poweluza milandu mumpingo.